Lyrics:
ChichewaSiyani dumboSiyani umbomboTatopa nazo kodi simukudziwa kuti lija ndi kale?Siya umbandaSiya zauchigawengaKodi watani iwe siukudziwa kuti kupha ndi sambi?Siyani dumboHear me nowHear me nowHear me nowHear me nowHear me nowHear me nowSiya kadukaSiya zokonda kubaSiyani chinyengo kuyambila lero tiyeni tikonze tsogoloSiyani kugonaSiya kugona tuloKunja kwacha kodi simukuona kuti dzuwa latuluka?Siya kadukaHear me nowHear me nowHear me nowHear me nowHear me nowHear me nowDzaka makumi asanuZatha kufika leroMpaka lero umphawiUkungophabe dzikoDzaka makumi asanuZatha kufika leroMpaka lero umphawiUkungophabe dziko