|
|
Songs | Albums | Album Arts
Lyrics:
Is hip-hop hereditary? I don't know Oh, the boys move fast You should take it slow Well, we all need someone to tell us when to go A beat-box imaginary in the show All you shell-toes lined up in a row All your favorite breaks Your favorite ELO
Musadabwe ndikamavina ine gule wakwathu uuuu Kum'mwera kwa Africa kule dziko limodzi lotchedwa Malawi iiii Warm heart of Africa kuli magule magule okoma aaaa Tchopa, manganje, ngoma, vimbuza, maseche ndi M'ganda aaaa
Zikomo zikomo nonse Kodi muli bwanji Ine ndili bwino ooooo Alendo asaononge Dziko la mtendere Malawi wabwino ooooo
Zikatere zikatere tiyeni tilowe m'bwalo Zikatere zikatere wayaka moto oo Zikatere zikatere pali ngozi pano Zikatere zikatere malawi moto oo
Oh please tell me when to go Iwe newo
|